Bwalo la Senior Resident Magistrate Joshua Nkhono ku Balaka lalamula kuti a Lilian Matako komanso a Ishmael Chitete akagwire ntchito zosalipidwa m'dera lawo atapezeka olakwa pa mlandu ovulaza munthu mwadala. Awiriwa adamangidwa zitadziwika kuti adapeleka chilango chomumangilira mumtengo mwana wa zaka zisanu ndi zinayi, Mercy Magombo, komanso kumuthira madzi a chitedze kaamba komuganizira kuti adaba […]
The post Matako apatsidwa chilango chogwira ntchito zosalipidwa appeared first on Malawi 24.