Bambo wa zaka 29, Edward Luka, wa m'mudzi mwa Madzedze Kaponda, ku Monkey Bay m’boma la Mangochi, wamwalira kamba komenyedwa ndi gule wamkulu wotchedwa kang’wing'wi yemwe adakumana naye pomwe amayendera zake. Lachinayi lapitali dzuwa likuswa mtengo, Luka amkapita ku nyumba kwake ndipo adangoti gululu ndi kangw'ingw'iyu. Kuyiwala kuti ukayendera mzengo usati asakhwi afumbura, kangw'ingw'iyu adayamba […]
The post Nyawu yapha munthu appeared first on Malawi 24.