A zaumoyo ku Zomba ati ophunzira wa ku sukulu ya ukachenjede ya Unima wagonekedwa mchipatala ku Zomba ndipo akuganiziridwa kuti ali ndi Cholera. Malingana ndi a Arnold Mndalirs omwe amayankhulira ofesi ya za umoyo ku Zomba, ophunzirayu yemwe amakhala ku Chikanda akuganiziridwa kuti ali ndi nthenda ya cholera. Pakali pano azachipatala amuyesa ndipo zotsatira zikuyembekezeka […]
The post Ophunzira ku Unima akuganiziridwa kuti ali ndi Cholera ku Zomba appeared first on Malawi 24.