Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera, yemwe omunyadira amangoti Lazaro, wadandaula kuti a Malawi akumamutumizira mauthenga omunyoza pa nambala yake ya WhatsApp kamba koti iye akulephera kuyendetsa dziko lino. Poyankhula pomwe amatsekulira ndondomeko ya chitukuko ku Lilongwe, A Chakwera anati pali anthu ena ambiri omwe amawatumizira mauthenga pa foni yawo kuwatukwana. Iwo anonjezera kunena kuti […]
The post Munditukwaniranji? Walira mokweza Lazaro appeared first on Malawi 24.