Moto wawotcha ofesi yowulutsilako mawu ndi zinthunzi ya kanema wa Luntha ku Lilongwe. Malingana ndi uthenga omwe akulu akulu ku wailesiyi atulutsa ati padakali pano sakudziwa chomwe chinayambitsa motowu. Iwo apitiliza kunena kuti motowu wawononga zinthu monga zojambulila, zotchinjila mawu kuti azimveka bwino komanso zomwe zimabweletsa mphepo yabwino mu ofesi mwawo. Kucha kwa lero anthu […]
The post Moto wawotcha wailesi yakanema ya Luntha appeared first on Malawi 24.