Unduna wa zachilengedwe kudzera mu nthambi yake yowona zanyengo yati kukhala kukutentha mzigawo zonse za dziko lino kuyambila lolemba kufikira lachinayi lino kaamba ka mphepo yotchedwa Mvuma yomwe yikhale yikuwomba pa nyanja ya Malawi. Kudzera mkalata yomwe nthambiyi yatulutsa yati, anthu akhale tcheru kuyambira la chisanu mpaka lamulungu mzigawo zonse kamba kakuti mvula yamkuntho yizakhala […]
The post Kutentha kupitilira sabata lino, atero a zanyengo appeared first on Malawi 24.