Dzulo apolisi amanga mtsogoleri wagulu lomenyelera ufulu wa anthu la Malawi First a Bon Kalindo pa Kamuzu Road m'boma la Salima. Malipoti akusonyeza kuti a Kalindo awamanga pa mlandu okhudza kufalitsa uthenga osayenera pamasamba a mchezo omwe mchingerezi umatchedwa kuti Cyber related crime. A Kalindo apita nawo ku likulu la nthambi ya polisi ku Area […]
The post Kalindo wamangidwanso appeared first on Malawi 24.