Loto la timu ya Arsenal likusanduka loto la chumba pomwe chomwe ikufuna mu English Premier League (EPL) chikuoneka chawatelera kuposa mlamba. Izi zili delo kutsatira mpata wa ma points 13 omwe ulipo tsopano kuti agwirane ndi Liverpool kutsatira masewelo omwe Arsenal yagwirana pakhosi 0-0 ndi Nottingham Forest pa bwalo la City usiku wathawu. Manchester United […]
The post EPL yayaka moto appeared first on Malawi 24.