Mnyamata amene amadziwika bwino ndi dzina loti iPhone Daddy patsamba la mchezo la TikTok, Innocent Sengimana wazaka 23, wamangidwa ndi apolisi ku Area 3 munzinda wa Lilongwe kamba kobera anthu ndalama zokwana 5 miliyoni kwacha powanamiza kuti awapatsa lamya za mtundu wa iPhone 13. Mneneli wa apolisi ku Lilongwe a Hastings Chigalu atsimikiza zankhaniyi ndipo […]
The post Apolisi amanga nyamata wama iPhone appeared first on Malawi 24.