Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wati chilowele iwo m'boma m'chaka cha 2020, amanga ndipo akumangabe zitukuko zoposa 600 ndipo posachedwa atulutsa mndandanda wa zomangamanga zomwe achita kuti aMalawi aweluze mtunda omwe asuntha mzaka zinayi. Mtsogoleriyu wati dziko likamayandikira kupita ku masankho kumachuluka bodza. Iwo ati chitukuko cha dziko lathunthu sichimangidwa ndi ulamuliro umodzi, ponena […]
The post Zitukukuko zomwe tamanga zikuposa 600 - Chakwera appeared first on Malawi 24.