Mtsogoleri wa chipani cha Mzika Coalition, Milward Tobias, wapempha a Malawi kuti asatope pofuna kuthana ndi mavuto a zachuma omwe ali mu dziko muno. Izi zayankhulidwa pamene dziko lino likukumbukira amatiliti amene anamenyera ufulu kuti dziko lino kuti likhale loima palokha. Mu chikalata chomwe watulutsa, Mtsogoleriyu wati dziko lino likuyenera kukhala ndi chidwi kwambiri pakumanga […]
The post Tiyeni timenyebe nkhondo yolimbana mavuto a zachuma, watero Tobias appeared first on Malawi 24.