Poyenda mtaunimu kumayenda osamalitsa, penanso olo mutatsinzina kumene. Pali chiopsezo choti amayi a chipani chotsutsa cha DPP tsiku lina mutha kukumanizana nawo adakali chibadwire. Amayi otsatira chipani cha DPP ndinso mtsogoleri wakale a Peter Mutharika ati ayenda mbulanda kupita kunyumba ya boma ngati lingaliro lofuna kumunjata Peter Mutharika lingapitilire. Amayiwa anena izi pa nkumano wawo […]
The post Tiyenda maliseche - aopseza amayi a DPP appeared first on Malawi 24.