Ogwira ntchito za umoyo mdziko muno achenjeza kuti ayamba kachikena kunyanyala ntchito mu zipatala zonse za boma mdziko muno. Izi zikudza pomwe bungwe la oimila ogwira ntchito za umoyo-wa la Physician Assistant Union Of Malawi linati silokhutila kuti boma likulephera kukweza ndalama za alawansi mofanana ndi momwe anagwirizana ndi akuluakulu aku unduna wa za umoyo. […]
The post Tiyambaso kunyanyala ntchito, ogwira ntchito za umoyo muzipatala za boma awopseza mabwana awo appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.