Thupi la wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima kuphatikiza matupi ena a anthu asanu ndi anayi omwe amwalira pa ngozi ya ndege yomwe yachitika Lolemba mu nkhalango ya Chikangawa m'boma la Mzimba lafika pa bwalo la ndege la Kumuzu International Airports(KIA) mzinda wa Lilongwe. Matupiwa afika kudzera pa ndege za a silikari […]
The post Thupi la a Chilima ndi ena afika tsopano mu mzinda wa Lilongwe appeared first on Malawi 24.