Nduna yofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu ati thupi la wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima akaika ku mudzi kwawo ku Nsipe m'boma la Ntcheu Lolemba sabata ya mawa. Poyankhura pa msonkhano wa atolankhani lero ku Lilongwe , a Kunkuyu ati mwambo onse udzayambira ku bwalo lamasewero la Civo Lachisanu ndipo Lamulungu, thupili […]
The post Thupi la a Chilima lilowa m'manda Lolemba ku Nsipe appeared first on Malawi 24.