Dziko la Equatorial Guinea lachotsa ntchito a Baltasar Ebang Engonga ngati mkulu wa National Financial Investigation Agency (ANIF) kutsatira kutchuka kwa makanema awo pa masamba a m'chezo. A Ebanga atchuka pa masamba a m'chezo ndi makanema osakhala bwino, omwe amachita zachisembwere ndi azimayi osiyanasiyana mu office yawo komanso mahotela. M'tsogoleri wa Dziko la Equatorial Guinea […]
The post Tchamani wamapakulidwe osakhala bwino wachotsedwa ntchito ku Equatorial Guinea appeared first on Malawi 24.