Oyimba komanso kukanyanga nsambo mu chamba cha Reggea Jah Rhyno yemwe dzina lake lenileni ndi Hope Chiusiwa wa mugulu la Tuff Lions wati ayitanidwa kachiwiri ku kayimba ku Tanzania ku Zanzibar Festival mu August, chifukwa Reggae yawo sasungunula ngati sobo. Malingana ndi Rhyno, sichilichonse chomwe chimamveka ndi zin'gwenyen'gwenye zonga reggae nde kuti ndi reggae. 'Anthu […]
The post Reggae sasungunula ngati Sobo - Jah Rhyno appeared first on Malawi 24.