Reserve Bank of Malawi (RBM), yomwe ndi banki yayikulu m'dziko muno, yachenjeza kuti ithana ndi aliyense amene apezeke akukana ndalama ponena kuti inatha mphamvu ndipo potsindika za nkhaniyi a RBM ati ngakhale ma 1 tambala ndi ovomerezeka kugulira chinthu. Malingana ndi mneneri wa bankiyi, Dr Mark Lungu wati a Malawi akuyenera azipanga lipoti munthu amene […]
The post RBM yati ithana ndi amalonda amene amakana ndalama zina ponena kuti zidatha mphamvu appeared first on Malawi 24.