,Phungu wa chipani cha MCP kum’mwera kwa boma la Ntchisi, a Ulemu Chilapondwa, apepesa pa zomwe anayankhula dzulo kuti anthu akumudzi sadandaula za kukwera mtengo kwa mafuta ophikira. A Chilapondwa apepesa lero mu nyumba ya malamulo ku Lilongwe. Ku nyumba yamalamulo aphungu akukambirana zokhudza ndondomeko ya za chuma ya chaka chino kufika chaka cha mawa. […]
The post Phungu wa MCP wapepesa atanena kuti anthu akumudzi sadandaula za mafuta ophikira appeared first on Malawi 24.