A Yeremiah Chihana omwe ndi phungu wa m'dera la kumpoto m'boma la Mzimba adandaulidwa ndi anthu 24 omwe amawagwirila ntchito kamba koti anaphwanya pangano la ndalama zomwe amayenera kuwalipira. Anthuwa omwe pakadali pano akuswera pa ofesi ya za ntchito m'bomali ayenda mtunda wa makilomita 80 kuchokera ku Geza Mbalachanda pomwe akuyesetsa kupeza mayendedwe obwelera ku […]
The post Phungu aphwanya pangano pa kalipilidwe ka antchito ake appeared first on Malawi 24.