A George Chaponda mtsogoleri wa mbali yotsutsa boma mnyumba ya malamulo, ati akupepesa onse amene anabwera lachisanu kudzamvera State of the Nation Address (SONA) yomwe a mtsogoleri wa dziko Lazarus Chakwera anapeleka. A Chaponda ati anthuwo akanatha kutenga nthawi yawo kupanga zinthu zaphindu ku madela awo kuposa kumvera za ndale zomwe a Lazarus Chakwera amanena […]
The post Pepani aMalawi, a Chakwera anakutaitsani nthawi - Chaponda appeared first on Malawi 24.