Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wati ululu wa kukwera kwa mitengo ya zinthu mdziko lino bwezi uli owonjeza pakadapanda alimi a fodya pomwe wati otsutsa akanalimbikitsa ulimi wafodya osati ziwonetselo bwezi Malawi atapita patali. Pakali pano, mtengo okwera wagona pa $3.2 ndipo $1.2 otsikitsitsa. Poyankhula pa mwambo otsekulira msika wa fodya ku Kanengo mu […]
The post Otsutsa akanalimbikitsa ulimi wa fodya osati ma demo bwezi tili patali - Chakwera appeared first on Malawi 24.