Nduna ya za chuma a Symplex Chithyola Banda yauza nyumba ya Malamulo kuti dziko lino pofika September, 2024 linali ndi ngongole yosachepera K16.19 trillion ku maiko a kunja. Pa chifukwa ichi, mzika za dziko lino zomwe ndi zopyola 20 miliyoni, aliyese ali ndi udindo obweza ngongole ku maiko a kunja ndalama yoposera K809,500 kuti dziko […]
The post Nzika iliyonse ya dziko lino ili ndi ngongole yosachepera K809,500 ku maiko akunja appeared first on Malawi 24.