Ntchito yokonza msika wa Kamba munzinda wa Blantyre kukhala wa makono (shopping mall), yayambika ndipo pomwe tinathamangira ku malowa lero Lolemba, tinapeza pamalopa pakudulidwa mitengo kusonyeza chiyambi cha ntchitoyi. Mbali inayi, anthu omwe amachita malonda awo panja pa msikawu anali akusamutsa katundu wawo kupita naye tsidya la nsewu komwe akuti apatsidwa ndi khonsolo kuti akhale […]
The post Ntchito yokonza msika wa Kamba yayambika appeared first on Malawi 24.