Komatu kulibe kupuma ku ma bwalo. Ili mkamwakamwa ya Dorothy Shonga osumira Mayi Easter Gondwe, a Joshua Chisa Mbele nawo awopseza kuti akamang'ala ku bwalo kuti a Gerald Kampanikiza akuwayipitsira mbiri. Malingana ndi zimene alemba pa tsamba lawo a Chisa Mbele, ati ngati sachotsa mauthenga owazembelera kuti iwo ndi kathyali. Mu sabatayi, kunamveka kuti bambo […]
The post Nkhondo yosumilana yavuta: naye Mneneri Chisa Mbele wapanikizana ndi Kampanikiza appeared first on Malawi 24.