Anthu ena a midzi ya group village head Kabiyo ku Ulongwe m'boma la Balaka, ati njala yafika posawuzana pomwe ati Chimanga akugula kapu K900 pomwe chigoba K9000. Malinga ndi ulendo omwe Malawi24 inali nawo Lolemba, kupita mu delari anthu ena ati akumasungunulabe juwisi wa ma pakete kuwiritsa kuti amwe ndi kugona. Kafukufuku wathu wapezanso kuti […]
The post Njala yafika posauzana ku Balaka appeared first on Malawi 24.