Pamene unduna wa zaumoyo ukuyembekeza kulandira katemera wa Johnson and Johnson, undunawu wachenjeza anthu mdziko kuti asalandile katemera wa Johnson and Johnson ngati analandirapo kale wa AstraZeneca. Mlembi Wamkulu mu Unduna wa Zaumoyo a Dr. Charles Mwansambo ndi omwe anena izi mu chikalata chomwe anatulutsa lachitatu. Katemera wa mtundu wa Johnson and Johnson yemwe waperekedwa […]
The post Ngati munalandira katemera wa AstraZeneca, musabaitsenso wa J&J appeared first on Malawi 24.