A Dalitso Kabambe omwe anaonetsa chidwi chokapikisana nawo pa udindo wa mtsogoleri wa Democratic Progress Party (DPP) ku konveshoni ikubwerayi, atuluka chipanichi. Kabambe yemwe analinso gavanala wa Reserve Bank ya Malawi, walengeza za kutuluka kwake mchipani chotsutsa cha DPP kudzera mukalata yomwe atulutsa lero Lolemba pa July 15, 2024. M'kalatayi iwo ati, “Nditaganizira mozama, ndaganiza […]
The post Ngalawa zikuduphidwa! Kabambe atuluka DPP appeared first on Malawi 24.