Oyimba Nepman yemwe dzina lake lenileni ndi Neppier Longwe wadzudzula oyimba anzake omwe akumaonetsera mkhalidwe wa nsanje mmayimbidwe a m'dziko muno. Nepman, yemwe padakali pano ali m'dziko la Zambia wayankhula chomwechi kudzera pa tsamba lake la mchezo la Facebook pomwe wati anthu amene akumuchitira nsanje wa anamupeza ndipo azamusiwa mmayimbidwe. Chomwe chatsitsa dzaye kuti njobvu […]
The post Nepman adzudzula oimba anzake za nsanje appeared first on Malawi 24.