Ofalitsa nkhani za chipani cha UTM a Felix Njawala ati malemu Patricia Shanil Dzimbiri asanamwalire adalemba mbiri yomwe iwo ankafuna kuti anthu omwe adzafike pa maliro awo adzatsatire. Iwo ati ndizokhudza kwambiri kuti mwa zina zomwe iwo amkafuna ndi zoti omwe adzayankhule pa Maliro awo adzakhale a Dr. saulos Klaus Chilima. Koma akuti izi ndi […]
The post Ndizopweteka kuti a Chilima salankhura pa mwambo uno monga momwe mayi Dzimbiri ankafunila - Njawala appeared first on Malawi 24.