M'neneri Shepherd Bushiri wati kugula kwa ndege ndi chimodzi mwa zifukwa zomwe dziko la South Africa lidamumangira pamodzi ndi mkazi wake ponena kuti sizimagwirizana ndi msinkhu wake. Iwo afotokoza izi mu gawo loyamba la macheza awo ndi Kanema wa Zodiak. Iwo ati moyo wawo ndi banja lawo mdziko la South Africa udali ovuta ndipo ichi […]
The post Ndinamangidwa ndi kuzunzidwa chifukwa chogula ndege - watero M'neneri Bushiri appeared first on Malawi 24.