Mayi Mary Chilima wati adakali ndi mafunso ochuluka pa zomwe zinachitika maola 24 ku Chikangawa komwe wachiwiri kwa m'tsogoleri wa dziko lino a Saulos Klaus Chilima ndi anthu ena 8 anafa pa ngozi ya ndege. 'Ndikadakonda nditadziwa zomwe zinachitika pomwe Saulos ndi anthu ena 8 anafa pa ngozi ya ndege. Kodi ndi chifukwa chani Saulos, […]
The post Ndidakali ndi mafunso ochuluka - Chilima appeared first on Malawi 24.