Wachiwiri kwa mtsogoleri w achipani cha Democratic Progressive (DPP) mchigawo cha pakati, a Alfred Gangata ati tsopano boma layamba kumanga anthu m'malo mothana ndi mavuto omwe dziko likukuna nawo pakadali pano. Polankhula pomwe amapita kunyumba kwawo kuchokera ku bwalo la milandu, a Gangata ati pakali pano boma likuwamanga ndi cholinga choti asapangitse misonkhano ndipo ati […]
The post Mwanditokosola - Gangata appeared first on Malawi 24.