Zina ukamva kamba anga mwala: Mwana wa nzika yothawa kwawo yemwenso sanakwane zaka 18, ali pandandanda okanyongedwa m’dziko la Somaliland kamba kopha m'modzi mwa anthu omwe ankafuna kumupanga chiwembu. Pa 11 February chaka chino, bwalo la milandu m’dziko la Somaliland linagamula Abshir Saleban Hussein wosakwana zaka 18, yemwe bambo ake anathawa m’dziko la Ethiopia kuti […]
The post Mwana ali pa ndandanda okaphedwa ku Somaliland appeared first on Malawi 24.