Mphunzitsi wa FCB Nyasa Big Bullets Peter Mponda walanda utsogoleri wa ukaputeni (Captain) mwa Clyde Senaji ndi kupeleka kwa Lloyd Aaron. Poyamba mphunzitsi Mponda anasankha Senaji ngati Captain koma m'masewelo angapo omwe amatenga utsogoleri pa amzake anali Àaron kapena Frank Willard. Mponda tsopano wasankhiratu osewera wapakatiyu ndipo omutsatira wake ndi Yankho Singo ndipo ngati awiriwa […]
The post Mponda walanda ukaputeni kwa Senaji kupeleka kwa Aaron appeared first on Malawi 24.