Moto olusa wawotcha sitolo ndi kupha anthu awiri a banja limodzi komanso kutentha ma sitololo oyandikirana nawo kwa Chemusa mu nzinda wa Blantyre lero. Malinga ndi mtsogoleri wa mu msikawu, a Hastings Kabango, banja lomwe lakumana ndi tsokali ndi la a Masina omwe amachita malonda ogulitsa zipangizo zosiyanasiyana (hardware). Apolisi atsimikiza za ngoziyi ndipo ati […]
The post Moto wapha anthu awiri kwa Chemusa appeared first on Malawi 24.