Magavanala a m'ma boma a chigawo chapakati mchipani cha UDF athetsa komiti yawo yayikulu mchigawochi ati chifukwa mamembala amakakamila ma udindo. Polankhula m'malo mwa magavanalawa pa msonkhano wawo ku Lilongwe masanawa, a Saidi Bauti anati ndiwokhumudwa ndi mene chipanichi chimasankhira adindo oyendetsa chipanichi mchigawochi. Iwo ati akhala akulembera akuluakulu achipanichi zokhudza nkhawa zawo kuyambira 2009 […]
The post Moto wabuka ku UDF! Magavanala a chigawo chapakati aphwasula komiti pawokha appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.