Mfumu Zatuwa ya m'boma la Kasungu yanjatidwa ndi a Polisi chifukwa choganiziridwa kuti yagwilirira mnzimayi wamisala m'munda wina wa chimanga muderalo. Malinga ndi m'neneri wa Polisi ku Kasungu Joseph Kachikho, mfumuyi inachita zoospazi m'mudzi mwa Kadongo m'dera la Mfumu yayikulu Chisanga m'bomalo. Kachikho wati pakhala pali malipoti kudelaro kuti mfumuyi yomwe dzina lake ndi Yohane […]
The post Mfumu yanjatidwa kamba kothetsela zilakolako zake pa mnzimayi wamisala appeared first on Malawi 24.