Apolisi kwa Mpingu m'boma la Lilongwe akusunga mchitolokosi mbusa wa mpingo wa Kadziyo Disciples, a Mccrystal Charlie a zaka 56, chifukwa chogonana ndi kuchimwitsa mtsikana wa zaka 16. Malingana ndi ofalitsa nkhani za apolisi ku Lilongwe a Hastings Chigalu, abusawa adagwa nalo mchikondi buthuli m'mwezi wa May chaka chatha pomwe limabwerabwera kudzatunga madzi pa m'jingo […]
The post M'busa atsindika malemba molakwika pa mwana wa zaka 16 appeared first on Malawi 24.