Kapena tiyambirenso ligi kapena, mwinatu ndi kubwela kwa Mzuzu City Hammers kapena. Ena a nyerere akuti ndi kusowa kwa ma penalty. Koma amene akuteteza chikho cha TNM Super League zikuoneka kuti sizinawayambire bwino ndithu. Atalepherana ndi timu ya Dedza Dynamos sabata latha mu masewero awo oyamba a ligi, timu ya Bullets yakanikananso ndi timu ya […]
The post Masewero awiri, ma pointi awiri - mtunda wa ligi utha kutalika kwa Bullets appeared first on Malawi 24.