Phungu wa ku Nyumba ya Malamulo dera la Chiradzulu West Mathews Ngwale, wadandaula kuti aphungu akayima kupempha zitukuko ku ma unduna, unduna ukakhala opanda mayankho umawabwezera nkhani ya chitukukocho kuti aphungu apite nayo ku khonsolo pomwe ati makhonsolo amakhala opanda ndalama komanso akuthandizidwa ndi chuma chosakwana. Phunguyu anayima kufunsa funso lowonjezera (supplementaly) pomwe anapempha kuti […]
The post Makhonsolo alibe ndalama - Ngwale appeared first on Malawi 24.