Komiti imene imawunikira anthu omwe ali oyenera kukapikisana nawo m'maudindo osiyanasiyana ku msonkhano waukulu wa chipani cha Malawi Congress (MCP) yati idalandira zikalata kuchokera kwa anthu 224 omwe adasonyeza chidwi pofuna kupikisana pa mipando yosiyanasiyana ku msonkhano waukulu wa chipanichi. Ngakhale izi zili chonchi, komitiyi yapeza kuti pa anthu 224 wa, 204 ndi amene ali […]
The post Maina ena asowa pa opikisana ku MCP appeared first on Malawi 24.