Apolisi ku Chileka munzinda wa Blantyre, anjata wonyamula mfuti mzawo pomuganizira kuti adachita nsipu wamera mukhola pa mayi wina yemwe adatsekeledwa mchitokosi cha polisi ya Lunzu. Usiku wa Lachiwiri laliwisili, Victor Kachingwe, adachita madyera mphoto pa Brenda Lyson wa zaka 20 yemwe adali muunyolo pa mlandu wina. Atalonjezedwa kuti zikatheka amasulidwa, Lyson adadzipeleka kuchita masewero […]
The post M’njati wanjatwa! appeared first on Malawi 24.