M'busa wina mu nzinda wa Lilongwe wamwalira pamene analowa mu m’tsinje wa Bua kuti azibatize yekha. Zadziwika kuti m’busayu dzina lake ndi Chisomo Duncan wa mpingo wa Ziyoni ndipo anapita kukabatiza nkhosa zake mu mtsinje wu. Malingana ndi zomwe otsatira a mpingowu adauza mneneri wa polisi m’chigawo chapakati chakunzambwe, a Foster Benjamin, m'busayu atamaliza kubatiza […]
The post M’busa amwalira pamene amazibatiza yekha appeared first on Malawi 24.