Nyimbo yoti chipatala cha Domasi Community m'boma la Zomba chitsekulidwa yakhala nyimbo yomwe yalira motopetsa. Phungu wa dera la Zomba Malosa a Grace Kwelepeta omwe lero mnyumba ya malamulo apemphanso unduna wa za umoyo kuti uganizire zotsekula gawo la OPD pa chipatalachi, ngakhale mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera mwezi wa July anati analandira […]
The post Kwelepeta wadandaulira boma kuti litsekule chipatala cha Domasi Community appeared first on Malawi 24.