Mkulu wa achinyamata mu chipani cha Democratic Progressive (DPP) a Norman Chisale achenjeza anthu ena omwe akulondalonda iwo komanso otsatira chipani cha DPP kuti tsiku lina adzabwezera, ndipo apolisi omwe adawombera m'modzi wa ma membala awo amudziwa ndipo adzamumanga pa 17 September. Poyankhula pamene amapelekeza a Alfred Gangata lero ku Lilongwe pomwe amatuluka mu chitolokosi […]
The post Kwakwana-kwakwana tiyeni tipatsane ulemu - Chisale appeared first on Malawi 24.