Nduna ya zamalonda, Vitumbiko Mumba wanenetsa kuti salora m'dziko muno kuchitika malonda osatsatira malamulo chifukwa chothandiza chipani ndi ndalama ngati chiphaso chochitira malondawa. Mwa zina, Mumba wanena kuti unduna wake uwonetsetsa kuti ochita malonda m'dziko muno akuchita malondawa motsata malamulo komaso mopindulira dziko lino. Iye ananena kuti pali amwenye ambiri amene amachita malonda awo mozembera […]
The post Kuthandiza chipani ndi ndalama si chiphaso chochitira malonda opanda chilorezo m'dziko muno - Mumba appeared first on Malawi 24.