Woyimba Jetu yemwe anayika khwimbi la a Malawi m'botolo, wapepesa kamba kotukwana mukanema ina yatsopano. Kuyambira Lachisanu, anthu m’masamba amchezo akhala akugawana kanema wina yemwe akuonetsa woyimba wa zaka 72-yu ali ndi mdzukulu wake pomwe amacheza ndi omutsatira ake kudzera pa kanema ya pompopompo (live video) pa tsamba lake la fesibuku. Macheza ali mkati, Jetu […]
The post Kunali kuphuluza chabe, Jetu apepesa potukwana appeared first on Malawi 24.