Kunali chipwilikiti ku Nyumba ya Malamulo kum'mawaku lero pomwe ena mwa anamandwa opanga malamulowa amafuna kuponyerana zibonyongo. Chatsitsa dzaye nchakuti pomwe Madalitso Kazombo, wachiwiri kwa sipikala wa nyumba ya malamuloyi analengeza kuti oyimilira aMalawi-wa akatchaye kaye mtentha ndebvu, Patricia Kainga Nangozo anathera mawu aphungu ambali yotsutsa boma. Kainga Nangozo yemwenso ndi wachiwiri kwa nduna yoona […]
The post Kunabukanso moto ku Nyumba ya Malamulo appeared first on Malawi 24.