Boma kudzera mu unduna wa zamalimidwe lalangiza anthu kuti asamale chakudya chomwe ali nacho chifukwa ulosi ukusonyeza kuti kuli nga’mba mu chaka cha ulimi cha 2023/24 zomwe zingathe kupangitsa kuchepa kwa chakudya pakhomo. Mlembi mu Unduna wa malimidwe a Dickxie V. Kampani ndi omwe anena izi potsatira ulosi wa nyengo omwe watulutsidwa ndi nthambi yoona […]
The post Kuli ng’amba chaka chino, samalani chakudya mu nyengo ya khilisimasi, latero boma appeared first on Malawi 24.